Genesis 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Popeza mwadzera njira yodutsa kwa kapolo wanu, mundilole ndikukonzereni kachakudya kuti mutsitsimutse mitima yanu.+ Mukatero mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.” Aroma 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gawanani ndi oyera malinga ndi zosowa zawo.+ Khalani ochereza.+
5 Popeza mwadzera njira yodutsa kwa kapolo wanu, mundilole ndikukonzereni kachakudya kuti mutsitsimutse mitima yanu.+ Mukatero mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.”