Genesis 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wake woyamba ndi Uza, ndi Buza+ m’bale wake, komanso Kemueli bambo ake a Aramu.