Salimo 119:100 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 100 Ndimachita zinthu mozindikira kuposa anthu achikulire,+Chifukwa ndimasunga malamulo anu.+ 1 Akorinto 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mukuona mmene anakuitanirani, abale, kuti si ambiri amene anthu amawaona kuti ndi anzeru+ omwe anaitanidwa,+ si ambiri amphamvu+ amene anaitanidwa, si ambiri a m’mabanja achifumu.
26 Mukuona mmene anakuitanirani, abale, kuti si ambiri amene anthu amawaona kuti ndi anzeru+ omwe anaitanidwa,+ si ambiri amphamvu+ amene anaitanidwa, si ambiri a m’mabanja achifumu.