Yeremiya 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitamande chifukwa cha nzeru zake.+ Munthu wamphamvu asadzitamande chifukwa cha mphamvu zake.+ Munthu wachuma asadzitamande chifukwa cha chuma chake.”+ 1 Akorinto 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 kuti pasapezeke munthu wodzitama+ pamaso pa Mulungu.
23 Yehova wanena kuti: “Munthu wanzeru asadzitamande chifukwa cha nzeru zake.+ Munthu wamphamvu asadzitamande chifukwa cha mphamvu zake.+ Munthu wachuma asadzitamande chifukwa cha chuma chake.”+