Mateyu 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma inu musamatchulidwe kuti Rabi, chifukwa mphunzitsi wanu ndi mmodzi yekha,+ ndipo nonsenu ndinu abale. Luka 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+
8 Koma inu musamatchulidwe kuti Rabi, chifukwa mphunzitsi wanu ndi mmodzi yekha,+ ndipo nonsenu ndinu abale.
19 Yesu anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+