Yobu 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi chiyembekezo cha wampatuko n’chiyani Mulungu akachotsa moyo wake,+Akamulanda moyo wake?+ Yobu 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma palibe wanena kuti, ‘Kodi Mulungu, Wondipanga Wamkulu,+ ali kuti,Amene amapatsa anthu nyimbo usiku?’+ Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+
10 Koma palibe wanena kuti, ‘Kodi Mulungu, Wondipanga Wamkulu,+ ali kuti,Amene amapatsa anthu nyimbo usiku?’+