Salimo 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Bwerani kuno ana anga, ndimvetsereni.+Ndikuphunzitsani kuopa Yehova.+