Salimo 49:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Moyo wake udzafanana ndi wa m’badwo wa makolo ake.+Ndipo iwo sadzaonanso kuwala.+