Yobu 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi Mulungu si wapamwamba kuposa kumwamba?+Onanso kuti nyenyezi+ zonse zili m’mwamba.