Miyambo 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 koma wolephera kundipeza akupweteka moyo wake.+ Onse odana ndi ine ndiye kuti amakonda imfa.”+ Miyambo 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati wakhala wanzeru, nzeruzo zidzapindulitsa iweyo.+ Ngati uli wonyoza, iweyo ndiye udzavutike.+ Yeremiya 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Kodi iwo akukhumudwitsa ine?’ watero Yehova.+ ‘Kodi iwo sakudzikhumudwitsa okha kuti achite manyazi pankhope zawo?’+
12 Ngati wakhala wanzeru, nzeruzo zidzapindulitsa iweyo.+ Ngati uli wonyoza, iweyo ndiye udzavutike.+
19 ‘Kodi iwo akukhumudwitsa ine?’ watero Yehova.+ ‘Kodi iwo sakudzikhumudwitsa okha kuti achite manyazi pankhope zawo?’+