Salimo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu mwaona mavuto ndi masautso.Mumawayang’anabe kuti muchitepo kanthu.+Waumphawi,+ mwana wamasiye,* amadziikiza m’manja mwanu.Inu mwakhala mthandizi wake.+ Salimo 140:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikudziwa bwino kwambiri kuti Yehova adzazengera+Mlandu anthu osautsika. Iye adzachitira chilungamo anthu osauka.+ Miyambo 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti Yehova adzawateteza pa mlandu wawo,+ ndipo adzalanda moyo wa amene akuwabera.+
14 Inu mwaona mavuto ndi masautso.Mumawayang’anabe kuti muchitepo kanthu.+Waumphawi,+ mwana wamasiye,* amadziikiza m’manja mwanu.Inu mwakhala mthandizi wake.+
12 Ndikudziwa bwino kwambiri kuti Yehova adzazengera+Mlandu anthu osautsika. Iye adzachitira chilungamo anthu osauka.+