1 Mafumu 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhalenso mahule aamuna a pakachisi ankapezeka m’dzikomo.+ Anthuwo anachita zinthu zonse zonyansa zimene inkachita mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+
24 Ngakhalenso mahule aamuna a pakachisi ankapezeka m’dzikomo.+ Anthuwo anachita zinthu zonse zonyansa zimene inkachita mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+