Miyambo 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wamkwiyo waukulu ayenera kulipitsidwa,+ chifukwa ukam’pulumutsa, uzichita zimenezi kawirikawiri.+ Miyambo 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wokonda kukwiya amayambitsa mkangano,+ ndipo aliyense wokonda kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+
22 Munthu wokonda kukwiya amayambitsa mkangano,+ ndipo aliyense wokonda kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+