Salimo 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Onse amene amakonda chilungamo changa afuule mosangalala ndi kukondwera.+Nthawi zonse azinena kuti:+“Alemekezeke Yehova, amene amasangalala mtumiki wake akakhala pa mtendere.”+ Salimo 69:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzatamanda dzina la Mulungu mwa kuimba nyimbo,+Ndipo ndidzamulemekeza ndi nyimbo zomuyamika.+ Luka 1:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Pamenepo Mariya anati: “Moyo wanga ukulemekeza Yehova.+
27 Onse amene amakonda chilungamo changa afuule mosangalala ndi kukondwera.+Nthawi zonse azinena kuti:+“Alemekezeke Yehova, amene amasangalala mtumiki wake akakhala pa mtendere.”+