2 Mbiri 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero, Yehova anapulumutsa Hezekiya ndi anthu okhala ku Yerusalemu m’manja mwa Senakeribu mfumu ya Asuri+ komanso m’manja mwa ena onse, ndipo anawapatsa mpumulo kwa adani awo onse owazungulira.+ Salimo 91:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+ Machitidwe 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Petulo nzeru zitamubwerera, anati: “Ndadziwa tsopano kuti Yehova ndiye watumiza mngelo wake+ kudzandilanditsa+ m’manja mwa Herode, komanso kudzandilanditsa ku zonse zimene anthu achiyuda anali kuyembekezera.”
22 Chotero, Yehova anapulumutsa Hezekiya ndi anthu okhala ku Yerusalemu m’manja mwa Senakeribu mfumu ya Asuri+ komanso m’manja mwa ena onse, ndipo anawapatsa mpumulo kwa adani awo onse owazungulira.+
15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+
11 Koma Petulo nzeru zitamubwerera, anati: “Ndadziwa tsopano kuti Yehova ndiye watumiza mngelo wake+ kudzandilanditsa+ m’manja mwa Herode, komanso kudzandilanditsa ku zonse zimene anthu achiyuda anali kuyembekezera.”