Salimo 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Moyo wathu wakhala ukuyembekeza Yehova.+Iye ndi mthandizi wathu ndi chishango chathu.+ Yesaya 42:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzanyamuka ngati munthu wamphamvu.+ Ngati wankhondo, iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri.+ Iye adzafuula, ndithu adzafuula mfuu yankhondo,+ ndipo adzakhala wamphamvu kuposa adani ake.+
13 Yehova adzanyamuka ngati munthu wamphamvu.+ Ngati wankhondo, iye adzachita zinthu modzipereka kwambiri.+ Iye adzafuula, ndithu adzafuula mfuu yankhondo,+ ndipo adzakhala wamphamvu kuposa adani ake.+