Salimo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikomereni mtima inu Yehova, pakuti ndasautsika kwambiri.+Diso langa lafooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso moyo wanga ndi m’mimba mwanga.+ Mateyu 26:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako anawauza kuti: “Moyo wanga ukumva chisoni chofa nacho.+ Khalani pompano ndipo mukhalebe maso pamodzi ndi ine.”+
9 Ndikomereni mtima inu Yehova, pakuti ndasautsika kwambiri.+Diso langa lafooka chifukwa cha chisoni,+ chimodzimodzinso moyo wanga ndi m’mimba mwanga.+
38 Kenako anawauza kuti: “Moyo wanga ukumva chisoni chofa nacho.+ Khalani pompano ndipo mukhalebe maso pamodzi ndi ine.”+