Salimo 73:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ndinachitira nsanje anthu odzitukumula,+Ndikamaona mtendere wa anthu oipa.+ Miyambo 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Usasirire munthu wachiwawa,+ kapena kusankha njira zake.+ Miyambo 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtima wako usamasirire anthu ochimwa,+ koma iwe uziopa Yehova tsiku lonse.+