Salimo 73:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa! Salimo 90:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Msipuwo umaphuka ndi kutsitsimuka m’mawa.+Madzulo umafota kenako umauma.+ Salimo 129:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzakhala ngati udzu wanthete womera padenga,+Umene umauma asanauzule,+
19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa!