Salimo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Perekani nsembe zachilungamo,+Ndipo khulupirirani Yehova.+ Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+ Yesaya 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndani pakati panu amene amaopa+ Yehova ndi kumvera mawu a mtumiki wake?+ Ndani amayenda mu mdima wokhawokha+ ndipo alibe kuwala? Iye akhulupirire dzina la Yehova+ ndipo adalire Mulungu wake.+ Aheberi 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso, musaiwale kuchita zabwino+ ndi kugawana zinthu ndi ena, pakuti nsembe zotero Mulungu amakondwera nazo.+
17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+
10 Ndani pakati panu amene amaopa+ Yehova ndi kumvera mawu a mtumiki wake?+ Ndani amayenda mu mdima wokhawokha+ ndipo alibe kuwala? Iye akhulupirire dzina la Yehova+ ndipo adalire Mulungu wake.+
16 Komanso, musaiwale kuchita zabwino+ ndi kugawana zinthu ndi ena, pakuti nsembe zotero Mulungu amakondwera nazo.+