Salimo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+
13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+