1 Samueli 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero Sauli anati: “Ndidzam’patsa Mikala kuti akhale msampha kwa iye,+ ndi kuti Afilisiti amuphe.” Zitatero Sauli anauza Davide kuti: “Lero uchite nane mgwirizano wa ukwati mwa kutenga mmodzi mwa akazi awiriwa.” Mateyu 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anali kupangana+ zoti agwire Yesu mochenjera ndi kumupha.
21 Chotero Sauli anati: “Ndidzam’patsa Mikala kuti akhale msampha kwa iye,+ ndi kuti Afilisiti amuphe.” Zitatero Sauli anauza Davide kuti: “Lero uchite nane mgwirizano wa ukwati mwa kutenga mmodzi mwa akazi awiriwa.”