Salimo 64:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene anola lilime lawo ngati lupanga,+Amene alunjikitsa mivi yawo, imene ndi mawu awo owawa,+