13 Inu ndinu woyera kwambiri moti simungaonerere zinthu zoipa ndipo simungathe kuonerera khalidwe loipa.+ N’chifukwa chiyani mumayang’ana anthu amene amachita zachinyengo,+ ndipo n’chifukwa chiyani mukupitiriza kukhala chete pamene munthu woipa akumeza munthu amene ndi wolungama kuposa iyeyo?+