2 Samueli 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Ahitofeli ataona kuti malangizo ake sanawagwiritse ntchito,+ anakwera bulu wake ndi kunyamuka kupita kunyumba yake kumzinda wakwawo.+ Kenako anakonzekeretsa banja lake+ ndipo anadzimangirira+ moti anafa.+ Chotero anaikidwa m’manda+ a makolo ake. Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha. Salimo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye wafukula dzenje, walikumbadi.+Koma adzagwera m’dzenje lokumba yekha.+ Salimo 35:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Awonongeke pamene iwo sakuyembekezera,+Akodwe mu ukonde umene atchera okha.+Agweremo ndi kuwonongeka.+
23 Koma Ahitofeli ataona kuti malangizo ake sanawagwiritse ntchito,+ anakwera bulu wake ndi kunyamuka kupita kunyumba yake kumzinda wakwawo.+ Kenako anakonzekeretsa banja lake+ ndipo anadzimangirira+ moti anafa.+ Chotero anaikidwa m’manda+ a makolo ake.
8 Awonongeke pamene iwo sakuyembekezera,+Akodwe mu ukonde umene atchera okha.+Agweremo ndi kuwonongeka.+