Salimo 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akuletsa nkhondo mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+Wathyola uta ndi kuduladula mkondo.+Ndipo watentha magaleta pamoto.+ Salimo 76:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kumeneko wathyola mivi yoyaka moto,+Wathyola chishango, lupanga ndi zida zankhondo.+ [Seʹlah.]
9 Akuletsa nkhondo mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+Wathyola uta ndi kuduladula mkondo.+Ndipo watentha magaleta pamoto.+