Miyambo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa mwachilungamo+ kuposa kukhala ndi zinthu zambiri koma mopanda chilungamo.+ Miyambo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+ 1 Timoteyo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi, kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ kumeneko limodzi ndi kukhala wokhutira ndi zimene tili nazo,+ ndi njiradi yopezera phindu lalikulu.+
8 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa mwachilungamo+ kuposa kukhala ndi zinthu zambiri koma mopanda chilungamo.+
9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+
6 Ndithudi, kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ kumeneko limodzi ndi kukhala wokhutira ndi zimene tili nazo,+ ndi njiradi yopezera phindu lalikulu.+