Deuteronomo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo mawu awa amene ndikukulamula lero azikhala pamtima pako,+ Salimo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+ Aheberi 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’maganizo mwawo ndi kuwalemba m’mitima yawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo+ ndipo iwo adzakhala anthu anga,’+ watero Yehova.
8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+
10 “‘Pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’maganizo mwawo ndi kuwalemba m’mitima yawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo+ ndipo iwo adzakhala anthu anga,’+ watero Yehova.