Salimo 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye amabisalira anthu pafupi ndi midzi.Amabisalira munthu wosalakwa ndi kumupha.+ ע [ʽAʹyin]Maso ake amafunafuna waumphawi.+ Luka 19:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo anali kuphunzitsa m’kachisimo tsiku ndi tsiku. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu anafunitsitsa kumupha.+ Machitidwe 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma chiwembu chawocho chinadziwika kwa Saulo. Komabe iwo anali kuyang’anira mosamala m’zipata zonse usana ndi usiku kuti amuphe.+
8 Iye amabisalira anthu pafupi ndi midzi.Amabisalira munthu wosalakwa ndi kumupha.+ ע [ʽAʹyin]Maso ake amafunafuna waumphawi.+
47 Ndipo anali kuphunzitsa m’kachisimo tsiku ndi tsiku. Koma ansembe aakulu, alembi ndi akuluakulu a anthu anafunitsitsa kumupha.+
24 Koma chiwembu chawocho chinadziwika kwa Saulo. Komabe iwo anali kuyang’anira mosamala m’zipata zonse usana ndi usiku kuti amuphe.+