Salimo 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yembekezera Yehova.+ Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+Yembekezera Yehova.+ Miyambo 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Salaza njira ya phazi lako,+ ndipo njira zako zonse zikhazikike.+ Miyambo 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usanene kuti: “Ndidzabwezera choipa.”+ Khulupirira Yehova+ ndipo iye adzakupulumutsa.+