11 Ndiyeno Hamani anayamba kudzitamandira pamaso pawo chifukwa cha kuchuluka kwa chuma chake+ ndi kuchuluka kwa ana ake aamuna.+ Anadzitamandiranso chifukwa cha zonse zimene mfumu inamulemekeza nazo komanso chifukwa chakuti inamukweza kuposa akalonga ndi atumiki a mfumu.+