Nyimbo ya Solomo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Wachikondi wanga ndi wokongola ndipo khungu lake ndi lofiirira. Pa amuna 10,000, iye ndiye wooneka bwino kwambiri.+
10 “Wachikondi wanga ndi wokongola ndipo khungu lake ndi lofiirira. Pa amuna 10,000, iye ndiye wooneka bwino kwambiri.+