Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova. Salimo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Milomo yachinyengo isowe chonena,+Milomo imene ikulankhula motsutsana ndi wolungama,+ yosadziletsa pa kudzikweza ndi kunyoza ena.+ Luka 22:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Ndipo anapitiriza kunena zambiri zomunyoza.+
16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.
18 Milomo yachinyengo isowe chonena,+Milomo imene ikulankhula motsutsana ndi wolungama,+ yosadziletsa pa kudzikweza ndi kunyoza ena.+