Salimo 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo kumwamba kukunena za chilungamo chake,+Pakuti Mulungu ndiye Woweruza.+ [Seʹlah.] Aroma 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ayi! Koma Mulungu akhale wonena zoona,+ ngakhale kuti munthu aliyense angapezeke kukhala wonama,+ monganso Malemba amanenera kuti: “Mukamalankhula mumalankhula zachilungamo, kuti mupambane pamene mukuweruzidwa.”+
4 Ayi! Koma Mulungu akhale wonena zoona,+ ngakhale kuti munthu aliyense angapezeke kukhala wonama,+ monganso Malemba amanenera kuti: “Mukamalankhula mumalankhula zachilungamo, kuti mupambane pamene mukuweruzidwa.”+