Genesis 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Lero ndiye mukundipitikitsa pamalo ano ndi pamaso panu.+ Ndidzakhala woyendayenda+ ndi wothawathawa padziko lapansi, ndipo n’zoonekeratu kuti aliyense wondipeza, adzandipha ndithu.”+ 2 Mafumu 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Yehova anakomera mtima+ Aisiraeli ndi kuwachitira chifundo+ ndipo anatembenukira kwa iwo chifukwa cha pangano lake+ ndi Abulahamu,+ Isaki,+ ndi Yakobo.+ Iye sanafune kuwawononga+ ndipo sanawachotse pamaso pake mpaka lero. Salimo 102:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa cha kudzudzula kwanu kwamphamvu ndi mkwiyo wanu.+Inu mwandikweza m’mwamba kuti munditaye.+
14 Lero ndiye mukundipitikitsa pamalo ano ndi pamaso panu.+ Ndidzakhala woyendayenda+ ndi wothawathawa padziko lapansi, ndipo n’zoonekeratu kuti aliyense wondipeza, adzandipha ndithu.”+
23 Koma Yehova anakomera mtima+ Aisiraeli ndi kuwachitira chifundo+ ndipo anatembenukira kwa iwo chifukwa cha pangano lake+ ndi Abulahamu,+ Isaki,+ ndi Yakobo.+ Iye sanafune kuwawononga+ ndipo sanawachotse pamaso pake mpaka lero.
10 Chifukwa cha kudzudzula kwanu kwamphamvu ndi mkwiyo wanu.+Inu mwandikweza m’mwamba kuti munditaye.+