Salimo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, mfumu ikukondwera mu mphamvu zanu.+Ndipo idzapitiriza kukondwera mu chipulumutso chanu.+ Luka 1:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo mzimu wanga sungaleke kusefukira+ ndi chimwemwe mwa Mulungu, Mpulumutsi wanga.+
21 Inu Yehova, mfumu ikukondwera mu mphamvu zanu.+Ndipo idzapitiriza kukondwera mu chipulumutso chanu.+