Salimo 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yembekezera Yehova.+ Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+Yembekezera Yehova.+ Salimo 54:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzapereka nsembe kwa inu mofunitsitsa.+Inu Yehova, ndidzatamanda dzina lanu pakuti ndi labwino.+ Salimo 123:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Monga mmene maso a atumiki amayang’anira dzanja la mbuye wawo,+Mmene maso a kapolo wamkazi amayang’anira dzanja la mbuye wake wamkazi,+Momwemonso, maso athu adzayang’ana kwa Yehova Mulungu wathu,+Kufikira atatikomera mtima.+ Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+
6 Ndidzapereka nsembe kwa inu mofunitsitsa.+Inu Yehova, ndidzatamanda dzina lanu pakuti ndi labwino.+
2 Taonani! Monga mmene maso a atumiki amayang’anira dzanja la mbuye wawo,+Mmene maso a kapolo wamkazi amayang’anira dzanja la mbuye wake wamkazi,+Momwemonso, maso athu adzayang’ana kwa Yehova Mulungu wathu,+Kufikira atatikomera mtima.+