2 Samueli 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Abisalomu anali kumuuza kuti: “Taona, nkhani yakoyi ili bwino ndipo ndi yosavuta. Koma mfumu ilibe aliyense woti amvetsere nkhani yakoyi.”+
3 Pamenepo Abisalomu anali kumuuza kuti: “Taona, nkhani yakoyi ili bwino ndipo ndi yosavuta. Koma mfumu ilibe aliyense woti amvetsere nkhani yakoyi.”+