Genesis 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mzindawo unatchedwa Babele,+ chifukwa kumeneko, Yehova anasokoneza chilankhulo cha anthu onse, ndipo Yehova anabalalitsira+ anthuwo padziko lonse lapansi. 2 Samueli 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako uthenga unafika kwa Davide wonena kuti: “Ahitofeli nayenso ali pakati pa anthu amene akukonza chiwembu+ pamodzi ndi Abisalomu.”+ Pamenepo Davide anati:+ “Inu Yehova!+ Chonde, sandutsani malangizo a Ahitofeli kuti akhale opusa.”+ 2 Samueli 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Husai anauza Abisalomu kuti: “Malangizo amene Ahitofeli wapereka ulendo uno sali bwino ayi!”+
9 Mzindawo unatchedwa Babele,+ chifukwa kumeneko, Yehova anasokoneza chilankhulo cha anthu onse, ndipo Yehova anabalalitsira+ anthuwo padziko lonse lapansi.
31 Kenako uthenga unafika kwa Davide wonena kuti: “Ahitofeli nayenso ali pakati pa anthu amene akukonza chiwembu+ pamodzi ndi Abisalomu.”+ Pamenepo Davide anati:+ “Inu Yehova!+ Chonde, sandutsani malangizo a Ahitofeli kuti akhale opusa.”+
7 Pamenepo Husai anauza Abisalomu kuti: “Malangizo amene Ahitofeli wapereka ulendo uno sali bwino ayi!”+