Yoswa 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova Mulungu wanu ndiye anali kuwathamangitsa pamaso panu,+ ndipo anawapitikitsa chifukwa cha inu. Pamenepo, inu munatenga malo awo monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulonjezerani.+ Salimo 138:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzakwaniritsa zolinga zimene ali nazo pa ine.+Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+Musasiye ntchito ya manja anu.+
5 Yehova Mulungu wanu ndiye anali kuwathamangitsa pamaso panu,+ ndipo anawapitikitsa chifukwa cha inu. Pamenepo, inu munatenga malo awo monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulonjezerani.+
8 Yehova adzakwaniritsa zolinga zimene ali nazo pa ine.+Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+Musasiye ntchito ya manja anu.+