1 Mbiri 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Imbirani Yehova, inu nonse okhala padziko lapansi!+Tsiku ndi tsiku lengezani chipulumutso chimene amapereka!+ Salimo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Muimbireni choimbira cha zingwe ndi mtima wonse ndi kufuula mosangalala.+
23 Imbirani Yehova, inu nonse okhala padziko lapansi!+Tsiku ndi tsiku lengezani chipulumutso chimene amapereka!+
3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Muimbireni choimbira cha zingwe ndi mtima wonse ndi kufuula mosangalala.+