Salimo 96:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Lengezani ulemerero wake pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndiponso ntchito zake zodabwitsa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+ Aroma 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+
3 Lengezani ulemerero wake pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndiponso ntchito zake zodabwitsa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+
9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+