Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 140:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Anola lilime lawo ndipo lakhala ngati la njoka.+

      M’milomo yawo muli poizoni wa mphiri.+ [Seʹlah.]

  • Aroma 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Mmero wawo ndi manda otseguka. Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.”+ “M’milomo yawo muli poizoni wa njoka.”+

  • Yakobo 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena