2 Samueli 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tonsefe tidzafa+ ndi kukhala ngati madzi otayika amene sawoleka. Koma Mulungu wakonza zinthu+ ndipo ali ndi zifukwa zothandiza kuti munthu wopitikitsidwa asapitirize kukhala wopitikitsidwa. Salimo 112:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+
14 Tonsefe tidzafa+ ndi kukhala ngati madzi otayika amene sawoleka. Koma Mulungu wakonza zinthu+ ndipo ali ndi zifukwa zothandiza kuti munthu wopitikitsidwa asapitirize kukhala wopitikitsidwa.
10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+