Salimo 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi, ubwino ndi kukoma mtima kosatha zidzanditsata masiku onse a moyo wanga.+Ndipo ine ndidzakhala m’nyumba ya Yehova mpaka kalekale.+ Salimo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,+Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+
6 Ndithudi, ubwino ndi kukoma mtima kosatha zidzanditsata masiku onse a moyo wanga.+Ndipo ine ndidzakhala m’nyumba ya Yehova mpaka kalekale.+
4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,+Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+