Salimo 65:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Inu Mulungu, anthu akukutamandani mu Ziyoni+ ndipo akhala chete pamaso panu,Iwo adzakwaniritsa malonjezo awo kwa inu.+
65 Inu Mulungu, anthu akukutamandani mu Ziyoni+ ndipo akhala chete pamaso panu,Iwo adzakwaniritsa malonjezo awo kwa inu.+