1 Mafumu 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Solomo anaimirira kutsogolo kwa guwa lansembe+ la Yehova pamaso pa mpingo wonse wa Isiraeli. Kenako anatambasula manja ake n’kuwakweza kumwamba.+ Salimo 134:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene mukupemphera mutakweza manja anu, muzikhala oyera,+Ndipo tamandani Yehova.+
22 Tsopano Solomo anaimirira kutsogolo kwa guwa lansembe+ la Yehova pamaso pa mpingo wonse wa Isiraeli. Kenako anatambasula manja ake n’kuwakweza kumwamba.+