1 Samueli 17:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandilanditsa m’kamwa mwa mkango ndi m’kamwa mwa chimbalangondo andilanditsanso m’manja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.”+ Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+ Salimo 54:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Mulungu ndiye mthandizi wanga.+Yehova ali pakati pa anthu amene akuchirikiza moyo wanga.
37 Ndiyeno Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandilanditsa m’kamwa mwa mkango ndi m’kamwa mwa chimbalangondo andilanditsanso m’manja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.”+
46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+