Salimo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.+Madalitso anu ali pa anthu anu.+ [Seʹlah.] Salimo 68:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Adalitsike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+Mulungu woona wa chipulumutso chathu.+ [Seʹlah.]
19 Adalitsike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+Mulungu woona wa chipulumutso chathu.+ [Seʹlah.]