Salimo 93:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+
93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+